Mateyu 13:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Munda ndiwo dziko+ ndipo mbewu zabwino ndi ana a ufumu. Koma namsongole ndi ana a woipayo,+