Mateyu 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Fosholo yake youluzira mankhusu* ili m’manja mwake, ndipo malo ake opunthirapo mbewu adzawayeretseratu kuti mbee! Tirigu adzamututira m’nkhokwe,+ koma mankhusu adzawatentha+ ndi moto umene sungazimitsidwe.” Luka 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Fosholo yake youluzira mankhusu* ili m’manja mwake. Akufuna kuyeretseratu mbee! malo ake opunthirapo mbewu ndi kututira+ tirigu munkhokwe yake. Koma mankhusu+ adzawatentha ndi moto+ umene sungazimitsidwe.”
12 Fosholo yake youluzira mankhusu* ili m’manja mwake, ndipo malo ake opunthirapo mbewu adzawayeretseratu kuti mbee! Tirigu adzamututira m’nkhokwe,+ koma mankhusu adzawatentha+ ndi moto umene sungazimitsidwe.”
17 Fosholo yake youluzira mankhusu* ili m’manja mwake. Akufuna kuyeretseratu mbee! malo ake opunthirapo mbewu ndi kututira+ tirigu munkhokwe yake. Koma mankhusu+ adzawatentha ndi moto+ umene sungazimitsidwe.”