1 Yohane 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amene amachitabe tchimo anachokera kwa Mdyerekezi, chifukwa Mdyerekezi wakhala akuchimwa kuyambira pa chiyambi.+ Choncho, Mwana wa Mulungu anaonekera+ kuti awononge ntchito za Mdyerekezi.+
8 Amene amachitabe tchimo anachokera kwa Mdyerekezi, chifukwa Mdyerekezi wakhala akuchimwa kuyambira pa chiyambi.+ Choncho, Mwana wa Mulungu anaonekera+ kuti awononge ntchito za Mdyerekezi.+