Mateyu 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma ataganiza mozama za nkhani imeneyi, mngelo wa Yehova* anamuonekera m’maloto n’kumuuza kuti: “Yosefe, mwana wa Davide, usaope kutengera Mariya mkazi wako kunyumba, chifukwa chakuti pakati alinapopa pachitika mwa mphamvu ya mzimu woyera.+ Mateyu 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Herode atamwalira, mngelo wa Yehova anaonekera kwa Yosefe m’maloto+ ku Iguputo
20 Koma ataganiza mozama za nkhani imeneyi, mngelo wa Yehova* anamuonekera m’maloto n’kumuuza kuti: “Yosefe, mwana wa Davide, usaope kutengera Mariya mkazi wako kunyumba, chifukwa chakuti pakati alinapopa pachitika mwa mphamvu ya mzimu woyera.+