-
Mateyu 2:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Kenako, Herode anaitanitsa mwamseri okhulupirira nyenyezi aja, ndipo atawafunsa mosamala, anadziwa nthawi yeniyeni imene nyenyeziyo inaonekera.
-