Mateyu 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komabe, ine ndikukuuzani kuti Eliya anabwera kale ndipo iwo sanamuzindikire koma anam’chitira zilizonse zimene iwo anafuna. Momwemonso iwo adzazunza Mwana wa munthu.”+ Maliko 6:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 n’kuubweretsa m’mbale, ndi kuupereka kwa mtsikana uja. Ndiyeno mtsikanayo anakaupereka kwa mayi ake.+
12 Komabe, ine ndikukuuzani kuti Eliya anabwera kale ndipo iwo sanamuzindikire koma anam’chitira zilizonse zimene iwo anafuna. Momwemonso iwo adzazunza Mwana wa munthu.”+
28 n’kuubweretsa m’mbale, ndi kuupereka kwa mtsikana uja. Ndiyeno mtsikanayo anakaupereka kwa mayi ake.+