Maliko 6:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Tsopano atawolokera kumtunda, anafika ku Genesarete ndi kuimika ngalawayo chapafupi.+ Yohane 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamenepo anamulandira m’ngalawa yawo, ndipo posapita nthawi ngalawa ija inakaima kumtunda kumene anali kupita.+
21 Pamenepo anamulandira m’ngalawa yawo, ndipo posapita nthawi ngalawa ija inakaima kumtunda kumene anali kupita.+