Maliko 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo pamene anaona ena mwa ophunzira ake akudya chakudya ndi manja oipitsidwa, kapena kuti, m’manja mosasamba*+ . . . Luka 11:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma Mfarisiyo anadabwa kuona kuti anayamba kudya chakudyacho asanasambe.+ Yohane 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamalopo panali mbiya zamwala zokwanira 6 malinga ndi malamulo a Ayuda a kudziyeretsa.+ Mbiya iliyonse inali ya malita pafupifupi 44 mpaka 66.
2 Ndipo pamene anaona ena mwa ophunzira ake akudya chakudya ndi manja oipitsidwa, kapena kuti, m’manja mosasamba*+ . . .
6 Pamalopo panali mbiya zamwala zokwanira 6 malinga ndi malamulo a Ayuda a kudziyeretsa.+ Mbiya iliyonse inali ya malita pafupifupi 44 mpaka 66.