Maliko 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nthawi yomweyo iye anakwera ngalawa pamodzi ndi ophunzira ake ndi kufika m’madera a Dalamanuta.+