Maliko 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tsopano Yesu ndi ophunzira ake anachoka ndi kupita kumidzi ya Kaisareya wa Filipi. Ali m’njira, anayamba kufunsa ophunzira ake, kuti: “Kodi anthu akumanena kuti ine ndine ndani?”+ Luka 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nthawi inayake, pamene anali kupemphera payekha, ophunzira ake anafika kwa iye onse pamodzi. Ndiyeno iye anawafunsa kuti: “Kodi anthuwa akumati ine ndine ndani?”+
27 Tsopano Yesu ndi ophunzira ake anachoka ndi kupita kumidzi ya Kaisareya wa Filipi. Ali m’njira, anayamba kufunsa ophunzira ake, kuti: “Kodi anthu akumanena kuti ine ndine ndani?”+
18 Nthawi inayake, pamene anali kupemphera payekha, ophunzira ake anafika kwa iye onse pamodzi. Ndiyeno iye anawafunsa kuti: “Kodi anthuwa akumati ine ndine ndani?”+