Yohane 1:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Choyamba iyeyu anapeza m’bale wake Simoni, ndi kumuuza kuti: “Ifetu tapeza Mesiya”+ (dzina lotanthauza, Khristu,+ polimasulira). Yohane 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pamenepo mayiyo anati: “Ndikudziwa kuti Mesiya+ akubwera, wotchedwa Khristu.+ Ameneyo akadzafika, adzatifotokozera zonse poyera.” Yohane 11:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iye anayankha kuti: “Inde, Ambuye. Ndimakhulupirira kuti ndinu Khristu Mwana wa Mulungu, Amene dziko linali kuyembekezera kubwera kwake.”+
41 Choyamba iyeyu anapeza m’bale wake Simoni, ndi kumuuza kuti: “Ifetu tapeza Mesiya”+ (dzina lotanthauza, Khristu,+ polimasulira).
25 Pamenepo mayiyo anati: “Ndikudziwa kuti Mesiya+ akubwera, wotchedwa Khristu.+ Ameneyo akadzafika, adzatifotokozera zonse poyera.”
27 Iye anayankha kuti: “Inde, Ambuye. Ndimakhulupirira kuti ndinu Khristu Mwana wa Mulungu, Amene dziko linali kuyembekezera kubwera kwake.”+