Maliko 9:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Koma aliyense wokhumudwitsa mmodzi wa tiana tokhulupirirati, zingakhale bwino kwambiri kuti amumangirire chimwala champhero m’khosi mwake, ngati chimene bulu amayendetsa, ndi kumuponya m’nyanja.+ Luka 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zingamuyendere bwino kwambiri atamukoloweka chimwala cha mphero m’khosi mwake ndi kumuponya m’nyanja,+ kusiyana n’kuti akhumudwitse mmodzi wa tiana iti.+
42 Koma aliyense wokhumudwitsa mmodzi wa tiana tokhulupirirati, zingakhale bwino kwambiri kuti amumangirire chimwala champhero m’khosi mwake, ngati chimene bulu amayendetsa, ndi kumuponya m’nyanja.+
2 Zingamuyendere bwino kwambiri atamukoloweka chimwala cha mphero m’khosi mwake ndi kumuponya m’nyanja,+ kusiyana n’kuti akhumudwitse mmodzi wa tiana iti.+