1 Akorinto 7:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndithudi, ndikufuna kuti mukhale opanda nkhawa.+ Mwamuna wosakwatira amadera nkhawa zinthu za Ambuye, mmene angakondweretsere Ambuye. 1 Akorinto 7:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Nayenso amene walekana ndi moyo wokhala yekha* n’kulowa m’banja wachita bwino,+ koma amene sanalowe m’banja wachita bwino koposa.+ 1 Akorinto 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tili ndi ufulu wotenga alongo amene ndi akazi athu+ pa maulendo, mmene amachitira atumwi ena onse ndiponso abale a Ambuye+ komanso Kefa,+ si choncho kodi?
32 Ndithudi, ndikufuna kuti mukhale opanda nkhawa.+ Mwamuna wosakwatira amadera nkhawa zinthu za Ambuye, mmene angakondweretsere Ambuye.
38 Nayenso amene walekana ndi moyo wokhala yekha* n’kulowa m’banja wachita bwino,+ koma amene sanalowe m’banja wachita bwino koposa.+
5 Tili ndi ufulu wotenga alongo amene ndi akazi athu+ pa maulendo, mmene amachitira atumwi ena onse ndiponso abale a Ambuye+ komanso Kefa,+ si choncho kodi?