Luka 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yesu anamufunsa kuti: “Kodi m’Chilamulo analembamo chiyani?+ Umawerengamo zotani?”