Maliko 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano nthawi ili cha m’ma 9 koloko m’mawa,*+ iwo anam’pachika. Machitidwe 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Sikuti anthu awa aledzera+ ngati mmene inu mukuganizira ayi, chifukwa nthawi panopa ndi 9 koloko m’mawa.*
15 Sikuti anthu awa aledzera+ ngati mmene inu mukuganizira ayi, chifukwa nthawi panopa ndi 9 koloko m’mawa.*