Mateyu 27:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Kuyambira cha m’ma 12 koloko masana* kunagwa mdima+ m’dziko lonselo, mpaka 3 koloko masana.*+