Maliko 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano pamene anali kuyandikira Yerusalemu, Betefage ndi Betaniya,+ ali paphiri la Maolivi, anatumiza ophunzira ake awiri+ Luka 19:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Tsopano atayandikira ku Betefage ndi Betaniya paphiri lotchedwa phiri la Maolivi,+ anatumiza ophunzira ake awiri.+
11 Tsopano pamene anali kuyandikira Yerusalemu, Betefage ndi Betaniya,+ ali paphiri la Maolivi, anatumiza ophunzira ake awiri+
29 Tsopano atayandikira ku Betefage ndi Betaniya paphiri lotchedwa phiri la Maolivi,+ anatumiza ophunzira ake awiri.+