2 Mafumu 9:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthuwo atamva zimenezi, msangamsanga aliyense anavula malaya ake+ n’kumuyalira pamasitepe popanda kanthu. Kenako anayamba kuliza malipenga,+ ndipo anali kunena kuti: “Yehu wakhala mfumu!”+ Luka 19:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pamene anali kuyenda,+ anthu anali kuyala malaya awo akunja mumsewu.+
13 Anthuwo atamva zimenezi, msangamsanga aliyense anavula malaya ake+ n’kumuyalira pamasitepe popanda kanthu. Kenako anayamba kuliza malipenga,+ ndipo anali kunena kuti: “Yehu wakhala mfumu!”+