Luka 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi ubatizo wa Yohane unali wochokera kumwamba kapena kwa anthu?”+ Yohane 1:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Inenso sindinali kumudziwa, koma Amene anandituma+ kudzabatiza m’madzi anandiuza kuti, ‘Ukadzaona mzimu ukutsika ndi kukhazikika pa munthu wina, ameneyo ndiye wobatiza ndi mzimu woyera.’+
33 Inenso sindinali kumudziwa, koma Amene anandituma+ kudzabatiza m’madzi anandiuza kuti, ‘Ukadzaona mzimu ukutsika ndi kukhazikika pa munthu wina, ameneyo ndiye wobatiza ndi mzimu woyera.’+