Mateyu 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Afarisiwo anatuluka ndi kukakonza chiwembu choti amuphe.+ Luka 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma iwo anapenga ndi mkwiyo ndipo anayamba kukambirana zoti amuchite Yesu.+ Yohane 11:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Choncho kuyambira tsiku limenelo anapangana kuti amuphe.+