Mateyu 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako mzimu unatsogolera Yesu kuchipululu+ kuti akayesedwe+ ndi Mdyerekezi.