Mateyu 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Mdyerekezi uja anamusiya,+ ndipo kunabwera angelo ndi kuyamba kum’tumikira.+