Luka 8:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “Pita kunyumba, ndipo ukafotokoze zimene Mulungu wakuchitira.”+ Munthu uja anapitadi, ndipo anali kufalitsa mumzinda wonsewo zimene Yesu anam’chitira.+
39 “Pita kunyumba, ndipo ukafotokoze zimene Mulungu wakuchitira.”+ Munthu uja anapitadi, ndipo anali kufalitsa mumzinda wonsewo zimene Yesu anam’chitira.+