Luka 8:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Yesu atabwerera ku Galileya, khamu la anthu linamulandira ndi manja awiri, chifukwa onse anali kumuyembekeza.+
40 Yesu atabwerera ku Galileya, khamu la anthu linamulandira ndi manja awiri, chifukwa onse anali kumuyembekeza.+