Luka 8:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Koma Yesu anati: “Wina wandigwira, chifukwa ndamva kuti mphamvu+ yatuluka mwa ine.”+