Mateyu 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako mwamsanga, Yesu analimbikitsa ophunzira ake kuti akwere ngalawa ndi kutsogola kupita kutsidya lina, pamene iye anali kuuza anthuwo kuti azipita kwawo.+ Yohane 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano anthuwo ataona zizindikiro zimene anachitazo, anayamba kunena kuti: “Mosakayika uyu ndi mneneri+ uja amene anati adzabwera padziko.”
22 Kenako mwamsanga, Yesu analimbikitsa ophunzira ake kuti akwere ngalawa ndi kutsogola kupita kutsidya lina, pamene iye anali kuuza anthuwo kuti azipita kwawo.+
14 Tsopano anthuwo ataona zizindikiro zimene anachitazo, anayamba kunena kuti: “Mosakayika uyu ndi mneneri+ uja amene anati adzabwera padziko.”