Yohane 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndipo Yesu atamuona akulira, ndi Ayuda amene anabwera naye pamodzi akuliranso, anadzuma povutika mumtima ndi kumva chisoni.+ Yohane 11:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma Yesu atadzumanso movutika mtima, anafika kumanda achikumbutsowo.+ Kwenikweni linali phanga, ndipo analitseka ndi chimwala.+
33 Ndipo Yesu atamuona akulira, ndi Ayuda amene anabwera naye pamodzi akuliranso, anadzuma povutika mumtima ndi kumva chisoni.+
38 Koma Yesu atadzumanso movutika mtima, anafika kumanda achikumbutsowo.+ Kwenikweni linali phanga, ndipo analitseka ndi chimwala.+