Mateyu 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ophunzira ake anawolokera kutsidya lina koma anaiwala kutenga mikate.+