Mateyu 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Mose ndi Eliya anaonekera kwa iwo akukambirana ndi Yesu.+ Luka 9:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndiyeno panaonekanso anthu awiri akukambirana naye. Anthu amenewa anali Mose ndi Eliya.+