Mateyu 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Ambuye, muchitire chifundo mwana wanga wamwamuna, chifukwa ndi wakhunyu ndipo akuvutika kwambiri. Amagwera pamoto kawirikawiri ndiponso amagwera m’madzi kawirikawiri.+
15 “Ambuye, muchitire chifundo mwana wanga wamwamuna, chifukwa ndi wakhunyu ndipo akuvutika kwambiri. Amagwera pamoto kawirikawiri ndiponso amagwera m’madzi kawirikawiri.+