-
Mateyu 8:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Koma chakumadzulo, anthu anamubweretsera anthu ambiri ogwidwa ndi ziwanda, ndipo iye anatulutsa mizimu imeneyo ndi mawu okha. Onse amene sanali kumva bwino m’thupi anawachiritsa.
-