Salimo 86:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti inu Yehova ndinu Mulungu wabwino+ ndipo ndinu wokonzeka kukhululuka.+Kukoma mtima kosatha kumene mumawasonyeza onse oitana pa inu ndi kwakukulu.+
5 Pakuti inu Yehova ndinu Mulungu wabwino+ ndipo ndinu wokonzeka kukhululuka.+Kukoma mtima kosatha kumene mumawasonyeza onse oitana pa inu ndi kwakukulu.+