Maliko 11:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma pamene anali kudutsa m’mamawa, anaona mkuyu uja utafota kale ndi mizu yomwe.+