Mateyu 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Poyankha Yesu anati: “Inenso ndikufunsani chinthu chimodzi. Mukandiuza chinthu chimenecho, inenso ndikuuzani ulamuliro umene ndimachitira zimenezi:+ Luka 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Poyankha Yesu anawauza kuti: “Inenso ndikufunsani funso limodzi, ndipo mundiyankhe:+
24 Poyankha Yesu anati: “Inenso ndikufunsani chinthu chimodzi. Mukandiuza chinthu chimenecho, inenso ndikuuzani ulamuliro umene ndimachitira zimenezi:+