-
Levitiko 14:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 “Tsopano pa tsiku la 8,+ iye azitenga nkhosa zazing’ono zamphongo ziwiri zopanda chilema, ndi nkhosa yaing’ono yaikazi + imodzi yopanda chilema, yosapitirira chaka chimodzi. Azitenganso ufa wosalala wokwana magawo atatu mwa magawo 10 a muyezo wa efa, monga nsembe yake ya mbewu+ yothira mafuta, ndi muyezo umodzi* wa mafuta.+
-