Mateyu 21:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Koma alimi aja anagwira akapolo ake aja ndipo mmodzi anam’menya, wina anamupha, wina anam’ponya miyala.+
35 Koma alimi aja anagwira akapolo ake aja ndipo mmodzi anam’menya, wina anamupha, wina anam’ponya miyala.+