Mateyu 21:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Alimiwo ataona mwanayo anayamba kukambirana kuti, ‘Eya, uyu ndiye wolandira cholowa.+ Bwerani, tiyeni timuphe ndi kutenga cholowa chakecho!’+ Luka 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Alimiwo atamuona anayamba kukambirana kuti, ‘Eya, uyu ndiye wolandira cholowa. Tiyeni timuphe kuti cholowacho chikhale chathu.’+
38 Alimiwo ataona mwanayo anayamba kukambirana kuti, ‘Eya, uyu ndiye wolandira cholowa.+ Bwerani, tiyeni timuphe ndi kutenga cholowa chakecho!’+
14 Alimiwo atamuona anayamba kukambirana kuti, ‘Eya, uyu ndiye wolandira cholowa. Tiyeni timuphe kuti cholowacho chikhale chathu.’+