Mateyu 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma Yesu, podziwa kuipa mtima kwawo, ananena kuti: “Onyenga inu! Bwanji mukundiyesa?+ Luka 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma Yesu anazindikira ndale zawo ndipo anawauza kuti:+