Mateyu 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Zinachitika chimodzimodzi kwa wachiwiri ndi wachitatu, mpaka kwa onse 7 aja.+ Luka 20:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako wachitatu anamutenga. Zinachitika chimodzimodzi kwa amuna onse 7 aja: onse anamwalira osasiya ana.+
31 Kenako wachitatu anamutenga. Zinachitika chimodzimodzi kwa amuna onse 7 aja: onse anamwalira osasiya ana.+