Mateyu 22:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma Yesu anawayankha kuti: “Mukulakwitsa chifukwa simudziwa Malemba kapena mphamvu ya Mulungu.+ Luka 20:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yesu anawayankha kuti: “Ana a m’nthawi* ino amakwatira+ ndi kukwatiwa.