Luka 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pamenepo anamufunsa kuti: “Mphunzitsi, kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti kwenikweni, ndipo chizindikiro chosonyeza kuti zili pafupi kuchitika n’chiyani?”+
7 Pamenepo anamufunsa kuti: “Mphunzitsi, kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti kwenikweni, ndipo chizindikiro chosonyeza kuti zili pafupi kuchitika n’chiyani?”+