Ekisodo 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho pita. Ine ndidzakhala nawe polankhula ndipo ndidzakuuza zonena.”+ Luka 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 chifukwa ine ndidzakuuzani mawu oti munene ndi kukupatsani nzeru, zimene otsutsa anu onse sadzatha kuzikana kapena kuzitsutsa.+ Machitidwe 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo Petulo, atadzazidwa ndi mzimu woyera,+ anawayankha kuti: “Olamulira anthu ndiponso akulu inu, Machitidwe 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma iwo sanathe kulimbana ndi nzeru+ zimene anasonyeza komanso mzimu woyera umene unali kumutsogolera pamene anali kulankhula.+
15 chifukwa ine ndidzakuuzani mawu oti munene ndi kukupatsani nzeru, zimene otsutsa anu onse sadzatha kuzikana kapena kuzitsutsa.+
8 Pamenepo Petulo, atadzazidwa ndi mzimu woyera,+ anawayankha kuti: “Olamulira anthu ndiponso akulu inu,
10 Koma iwo sanathe kulimbana ndi nzeru+ zimene anasonyeza komanso mzimu woyera umene unali kumutsogolera pamene anali kulankhula.+