Yesaya 53:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa cha kuvutika kwake, iye adzaona zabwino+ ndipo adzakhutira.+ Chifukwa cha zimene akudziwa, mtumiki wanga wolungamayo+ adzachititsa kuti anthu ambiri azionedwa olungama,+ ndipo adzasenza zolakwa zawo.+ Luka 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ataona chikhulupiriro chawo, anati: “Bwanawe, machimo ako akhululukidwa.”+ Luka 7:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Kenako anauza mayiyo kuti: “Machimo ako akhululukidwa.”+
11 Chifukwa cha kuvutika kwake, iye adzaona zabwino+ ndipo adzakhutira.+ Chifukwa cha zimene akudziwa, mtumiki wanga wolungamayo+ adzachititsa kuti anthu ambiri azionedwa olungama,+ ndipo adzasenza zolakwa zawo.+