Mateyu 24:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndithu ndikukuuzani kuti m’badwo uwu+ sudzatha wonse kuchoka kufikira zinthu zonsezi zitachitika. Luka 21:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndithu ndikukuuzani, M’badwo umenewu sudzatha wonse kuchoka, kufikira zinthu zonsezi zitachitika.+
32 Ndithu ndikukuuzani, M’badwo umenewu sudzatha wonse kuchoka, kufikira zinthu zonsezi zitachitika.+