Luka 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yesu anatumiza Petulo ndi Yohane kuti: “Pitani mukatikonzere+ pasika kuti tidye.”