Luka 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno munthu ameneyo akakusonyezani chipinda chachikulu cham’mwamba chokonzedwa bwino. Mukakonzere mmenemo.”+
12 Ndiyeno munthu ameneyo akakusonyezani chipinda chachikulu cham’mwamba chokonzedwa bwino. Mukakonzere mmenemo.”+