1 Akorinto 11:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti nthawi zonse+ pamene mukudya mkate umenewu ndi kumwa za m’kapu imeneyi, mukulengezabe imfa+ ya Ambuye, mpaka iye adzafike.+
26 Pakuti nthawi zonse+ pamene mukudya mkate umenewu ndi kumwa za m’kapu imeneyi, mukulengezabe imfa+ ya Ambuye, mpaka iye adzafike.+