Mateyu 26:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Pambuyo pake anabwerera kwa ophunzirawo n’kuwauza kuti: “Zoona nthawi ngati ino mukugona ndi kupumula! Taonani! Ola lakuti Mwana wa munthu aperekedwe m’manja mwa ochimwa layandikira.+
45 Pambuyo pake anabwerera kwa ophunzirawo n’kuwauza kuti: “Zoona nthawi ngati ino mukugona ndi kupumula! Taonani! Ola lakuti Mwana wa munthu aperekedwe m’manja mwa ochimwa layandikira.+