Mateyu 26:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Pamenepo mkulu wa ansembe anaimirira ndi kumufunsa kuti: “Kodi ukusowa choyankha? Kodi n’zoona zimene awa akukunenezazi?”+
62 Pamenepo mkulu wa ansembe anaimirira ndi kumufunsa kuti: “Kodi ukusowa choyankha? Kodi n’zoona zimene awa akukunenezazi?”+