Mateyu 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma pamene ansembe aakulu komanso akulu anali kumuneneza,+ iye sanayankhe chilichonse.+